Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 25:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Inu Mulungu wanga, chikhulupiriro changa chili mwa inu.+

      Musalole kuti ndichite manyazi.

      Adani anga asakondwere chifukwa cha masautso anga.+

  • Salimo 35:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Musalole kuti anthu amene amadana ndi ine popanda chifukwa akondwere ndi kusautsika kwanga.+

      Ndipo musalole kuti anthu amene amandida popanda chifukwa anditsinzinire diso.+

  • Salimo 38:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ine ndinati: “Ngati simundiyankha adani anga adzasangalala chifukwa cha kusautsika kwanga.+

      Phazi langa likaterereka,+ iwo adzadzikweza pamaso panga.”+

  • Maliro 1:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndikulirira zinthu zimenezi ngati mkazi.+ Maso anga ine! Maso anga akutuluka misozi.+

      Pakuti wonditonthoza, munthu woti anditsitsimule, ali kutali ndi ine.

      Ana anga asiyidwa+ popanda thandizo, pakuti mdani wanga wadzitukumula.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena