Salimo 137:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kumeneko, amene anatigwira ukapolo anatiuza kuti tiwaimbire nyimbo,+Ndipo otinyozawo anatipempha kuti tiwasangalatse.+ Iwo anati:“Tiimbireni imodzi mwa nyimbo za ku Ziyoni.”+ Yeremiya 50:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Babulo muitanireni oponya mivi ndi uta, onse okunga uta.+ Mangani misasa momuzungulira. Pasapezeke wothawa.+ Mubwezereni zimene anachita.+ Muchitireni zonse zimene iye anachita.+ Iye wachita zinthu modzikuza pamaso pa Yehova, pamaso pa Woyera wa Isiraeli.+
3 Kumeneko, amene anatigwira ukapolo anatiuza kuti tiwaimbire nyimbo,+Ndipo otinyozawo anatipempha kuti tiwasangalatse.+ Iwo anati:“Tiimbireni imodzi mwa nyimbo za ku Ziyoni.”+
29 “Babulo muitanireni oponya mivi ndi uta, onse okunga uta.+ Mangani misasa momuzungulira. Pasapezeke wothawa.+ Mubwezereni zimene anachita.+ Muchitireni zonse zimene iye anachita.+ Iye wachita zinthu modzikuza pamaso pa Yehova, pamaso pa Woyera wa Isiraeli.+