Salimo 137:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa kumeneko, anthu amene anatigwira ukapolo anatiuza kuti tiwaimbire nyimbo,+Amene ankatinyozawo ankafuna kuti tiwasangalatse. Iwo anati: “Tiimbireni nyimbo imodzi ya ku Ziyoni.” Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 137:3 Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 139-140
3 Chifukwa kumeneko, anthu amene anatigwira ukapolo anatiuza kuti tiwaimbire nyimbo,+Amene ankatinyozawo ankafuna kuti tiwasangalatse. Iwo anati: “Tiimbireni nyimbo imodzi ya ku Ziyoni.”