Maliro 3:64 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 64 Inu Yehova, mudzawabwezera mogwirizana ndi ntchito za manja awo.+ 2 Atesalonika 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chiweruzo cha Mulunguchi n’cholungama chifukwa akubwezera masautso kwa amene amakusautsani.+ Chivumbulutso 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 M’bwezereni monga mmene iye anachitira.+ M’chitireni mowirikiza kawiri. Ndithu, wirikizani kawiri zinthu zimene iyeyo anachita.+ M’kapu+ imene anaikamo chakumwa chosakaniza, ikanimo chakumwa chakecho+ kuwirikiza kawiri.+
6 M’bwezereni monga mmene iye anachitira.+ M’chitireni mowirikiza kawiri. Ndithu, wirikizani kawiri zinthu zimene iyeyo anachita.+ M’kapu+ imene anaikamo chakumwa chosakaniza, ikanimo chakumwa chakecho+ kuwirikiza kawiri.+