Yobu 34:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti iye amapereka mphoto kwa munthu wochokera kufumbi malinga ndi zochita zake,+Ndipo amam’bweretsera zinthu zogwirizana ndi njira yake. Salimo 28:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Muwabwezere mogwirizana ndi zochita zawo,+Mogwirizana ndi kuipa kwa zochita zawo.+Abwezereni mogwirizana ndi ntchito za manja awo.+Abwezereni zochita zawo.+ Yeremiya 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma Yehova wa makamu amaweruza mwachilungamo.+ Amafufuza impso ndi mtima.+ Inu Mulungu, ndiloleni ndione mukuwapatsa chilango, pakuti ine ndakufotokozerani mlandu wanga.+ 2 Timoteyo 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Alekizanda,+ wosula zinthu zamkuwa uja, anandichitira zoipa zambiri. Yehova adzamubwezera malinga ndi ntchito zake,+
11 Pakuti iye amapereka mphoto kwa munthu wochokera kufumbi malinga ndi zochita zake,+Ndipo amam’bweretsera zinthu zogwirizana ndi njira yake.
4 Muwabwezere mogwirizana ndi zochita zawo,+Mogwirizana ndi kuipa kwa zochita zawo.+Abwezereni mogwirizana ndi ntchito za manja awo.+Abwezereni zochita zawo.+
20 Koma Yehova wa makamu amaweruza mwachilungamo.+ Amafufuza impso ndi mtima.+ Inu Mulungu, ndiloleni ndione mukuwapatsa chilango, pakuti ine ndakufotokozerani mlandu wanga.+
14 Alekizanda,+ wosula zinthu zamkuwa uja, anandichitira zoipa zambiri. Yehova adzamubwezera malinga ndi ntchito zake,+