Salimo 28:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Muwabwezere mogwirizana ndi zochita zawo,+Mogwirizana ndi kuipa kwa zochita zawo.+Abwezereni mogwirizana ndi ntchito za manja awo.+Abwezereni zochita zawo.+ Salimo 62:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komanso kukoma mtima kosatha ndi kwanu, inu Yehova,+Pakuti inu mumabwezera aliyense mogwirizana ndi ntchito zake.+ Miyambo 24:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ukanena kuti: “Ifetu izi sitinali kuzidziwa,”+ kodi amene amafufuza mitima sazindikira zimenezo?+ Ndipo kodi amene amayang’anitsitsa moyo wako sadziwa zimenezo+ n’kubwezera munthu wochokera kufumbi mogwirizana ndi ntchito yake?+
4 Muwabwezere mogwirizana ndi zochita zawo,+Mogwirizana ndi kuipa kwa zochita zawo.+Abwezereni mogwirizana ndi ntchito za manja awo.+Abwezereni zochita zawo.+
12 Komanso kukoma mtima kosatha ndi kwanu, inu Yehova,+Pakuti inu mumabwezera aliyense mogwirizana ndi ntchito zake.+
12 Ukanena kuti: “Ifetu izi sitinali kuzidziwa,”+ kodi amene amafufuza mitima sazindikira zimenezo?+ Ndipo kodi amene amayang’anitsitsa moyo wako sadziwa zimenezo+ n’kubwezera munthu wochokera kufumbi mogwirizana ndi ntchito yake?+