Salimo 59:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chifukwa cha tchimo la pakamwa pawo, ndi mawu a pamilomo yawo.+Agwidwe chifukwa cha kunyada kwawo,+Chifukwa cha kutukwana ndi chinyengo zimene amachita mobwerezabwereza. Yeremiya 18:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 M’nyumba zawo mumveke kulira mukawabweretsera magulu achifwamba mwadzidzidzi,+ chifukwa andikumbira mbuna kuti andigwire ndipo anditchera misampha kuti akole mapazi anga.+ 2 Timoteyo 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Alekizanda,+ wosula zinthu zamkuwa uja, anandichitira zoipa zambiri. Yehova adzamubwezera malinga ndi ntchito zake,+
12 Chifukwa cha tchimo la pakamwa pawo, ndi mawu a pamilomo yawo.+Agwidwe chifukwa cha kunyada kwawo,+Chifukwa cha kutukwana ndi chinyengo zimene amachita mobwerezabwereza.
22 M’nyumba zawo mumveke kulira mukawabweretsera magulu achifwamba mwadzidzidzi,+ chifukwa andikumbira mbuna kuti andigwire ndipo anditchera misampha kuti akole mapazi anga.+
14 Alekizanda,+ wosula zinthu zamkuwa uja, anandichitira zoipa zambiri. Yehova adzamubwezera malinga ndi ntchito zake,+