1 Timoteyo 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ena mwa amenewa ndi Hemenayo+ ndi Alekizanda,+ ndipo ndawapereka kwa Satana+ kuti akalangidwa,* aphunzire kuti sayenera kulankhula zonyoza Mulungu.+
20 Ena mwa amenewa ndi Hemenayo+ ndi Alekizanda,+ ndipo ndawapereka kwa Satana+ kuti akalangidwa,* aphunzire kuti sayenera kulankhula zonyoza Mulungu.+