1 Mbiri 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa tsiku limeneli m’pamene Davide anathandiza+ nawo kuyamika+ Yehova kudzera mwa Asafu+ ndi abale ake kwanthawi yoyamba, ndi nyimbo yakuti: Salimo 28:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova ndiye mphamvu yanga+ ndi chishango changa.+Mtima wanga umam’khulupirira.+Iye wandithandiza, moti mtima wanga ukukondwera.+Ndidzamutamanda mwa kumuimbira nyimbo yanga.+ Salimo 69:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndidzatamanda dzina la Mulungu mwa kuimba nyimbo,+Ndipo ndidzamulemekeza ndi nyimbo zomuyamika.+ Yesaya 35:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu owomboledwa ndi Yehova adzabwerera+ n’kukafika ku Ziyoni akufuula mosangalala.+ Iwo azidzasangalala mpaka kalekale.+ Adzakhala okondwa ndi osangalala ndipo chisoni ndi kubuula zidzachoka.+
7 Pa tsiku limeneli m’pamene Davide anathandiza+ nawo kuyamika+ Yehova kudzera mwa Asafu+ ndi abale ake kwanthawi yoyamba, ndi nyimbo yakuti: Salimo 28:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova ndiye mphamvu yanga+ ndi chishango changa.+Mtima wanga umam’khulupirira.+Iye wandithandiza, moti mtima wanga ukukondwera.+Ndidzamutamanda mwa kumuimbira nyimbo yanga.+ Salimo 69:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndidzatamanda dzina la Mulungu mwa kuimba nyimbo,+Ndipo ndidzamulemekeza ndi nyimbo zomuyamika.+ Yesaya 35:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu owomboledwa ndi Yehova adzabwerera+ n’kukafika ku Ziyoni akufuula mosangalala.+ Iwo azidzasangalala mpaka kalekale.+ Adzakhala okondwa ndi osangalala ndipo chisoni ndi kubuula zidzachoka.+
7 Yehova ndiye mphamvu yanga+ ndi chishango changa.+Mtima wanga umam’khulupirira.+Iye wandithandiza, moti mtima wanga ukukondwera.+Ndidzamutamanda mwa kumuimbira nyimbo yanga.+
10 Anthu owomboledwa ndi Yehova adzabwerera+ n’kukafika ku Ziyoni akufuula mosangalala.+ Iwo azidzasangalala mpaka kalekale.+ Adzakhala okondwa ndi osangalala ndipo chisoni ndi kubuula zidzachoka.+