Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 22:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Davide analankhula ndi Yehova mawu a nyimbo iyi,+ pa tsiku limene Yehova anamulanditsa kwa adani ake+ onse ndiponso m’manja mwa Sauli.+

  • 2 Samueli 23:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Mawu omaliza amene Davide ananena ndi awa:+

      “Mawu a Davide mwana wa Jese,+

      Mawu a munthu wamphamvu amene anakwezedwa pamwamba,+

      Wodzozedwa+ wa Mulungu wa Yakobo,

      Munthu wosangalatsa wotchulidwa m’nyimbo zokoma+ za Isiraeli.

  • 1 Mbiri 16:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndiyeno Davide anaika Alevi+ ena kukhala otumikira+ pa likasa la Yehova kuti azikumbutsa+ anthu, kuyamika,+ ndi kutamanda+ Yehova Mulungu wa Isiraeli.

  • 2 Akorinto 9:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Zili choncho chifukwa utumiki wothandiza anthu umenewu si kuti ukungopatsa oyerawo zinthu zochuluka zimene akufunikira,+ koma ukuchititsanso anthu ambiri kupereka mapemphero ochuluka oyamika Mulungu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena