1 Mbiri 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Muimbireni,+ muimbireni nyimbo zomutamanda!+Sinkhasinkhani ntchito zake zonse zodabwitsa.+ Amosi 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu mukupeka nyimbo zoti muziimba ndi zipangizo za zingwe,+ ndipo mofanana ndi Davide, mukupanga zipangizo zoimbira.+
5 Inu mukupeka nyimbo zoti muziimba ndi zipangizo za zingwe,+ ndipo mofanana ndi Davide, mukupanga zipangizo zoimbira.+