2 Samueli 22:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 N’chifukwa chake ndidzayamika inu Yehova pakati pa mitundu.+Ndipo ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.+ 2 Samueli 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mawu omaliza amene Davide ananena ndi awa:+“Mawu a Davide mwana wa Jese,+Mawu a munthu wamphamvu amene anakwezedwa pamwamba,+Wodzozedwa+ wa Mulungu wa Yakobo,Munthu wosangalatsa wotchulidwa m’nyimbo zokoma+ za Isiraeli.
50 N’chifukwa chake ndidzayamika inu Yehova pakati pa mitundu.+Ndipo ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.+
23 Mawu omaliza amene Davide ananena ndi awa:+“Mawu a Davide mwana wa Jese,+Mawu a munthu wamphamvu amene anakwezedwa pamwamba,+Wodzozedwa+ wa Mulungu wa Yakobo,Munthu wosangalatsa wotchulidwa m’nyimbo zokoma+ za Isiraeli.