Rute 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Obedi anabereka Jese,+ ndipo Jese anabereka Davide.+ 1 Samueli 17:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Ndiyeno Sauli anamufunsa kuti: “Mnyamata iwe, bambo wako ndani?” Poyankha Davide anati: “Ndine mwana wa mtumiki wanu Jese,+ wa ku Betelehemu.”+ Mateyu 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Jese anabereka mfumu+ Davide.+ Davide anabereka Solomo,+ yemwe mayi ake anali mkazi wa Uriya.
58 Ndiyeno Sauli anamufunsa kuti: “Mnyamata iwe, bambo wako ndani?” Poyankha Davide anati: “Ndine mwana wa mtumiki wanu Jese,+ wa ku Betelehemu.”+