Rute 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo akazi okhala naye pafupi+ anatcha mwanayo dzina lakuti Obedi.+ Ndipo iwo anati: “Mwana wabadwa kwa Naomi.” Obedi ndiye bambo ake a Jese,+ bambo ake a Davide. 1 Mbiri 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 wa 6 Ozemu, ndipo wa 7 anali Davide.+
17 Pamenepo akazi okhala naye pafupi+ anatcha mwanayo dzina lakuti Obedi.+ Ndipo iwo anati: “Mwana wabadwa kwa Naomi.” Obedi ndiye bambo ake a Jese,+ bambo ake a Davide.