1 Samueli 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano Davide anali mwana wamwamuna wa Jese, Mwefurata+ wina wa ku Betelehemu, ku Yuda. Jese anali ndi ana aamuna 8+ ndipo m’masiku a Sauli iye anali atakalamba kale. Yesaya 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nthambi+ idzatuluka pachitsa cha Jese,+ ndipo mphukira+ yotuluka pamizu yake idzakhala yobereka zipatso.+ Aroma 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komanso Yesaya anati: “Padzakhala muzu wa Jese,+ ndipo padzatuluka wina wodzalamulira mitundu.+ Mitundu idzayembekezera iye.”+
12 Tsopano Davide anali mwana wamwamuna wa Jese, Mwefurata+ wina wa ku Betelehemu, ku Yuda. Jese anali ndi ana aamuna 8+ ndipo m’masiku a Sauli iye anali atakalamba kale.
11 Nthambi+ idzatuluka pachitsa cha Jese,+ ndipo mphukira+ yotuluka pamizu yake idzakhala yobereka zipatso.+
12 Komanso Yesaya anati: “Padzakhala muzu wa Jese,+ ndipo padzatuluka wina wodzalamulira mitundu.+ Mitundu idzayembekezera iye.”+