-
Mateyu 1:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Jese anabereka mfumu+ Davide.+
Davide anabereka Solomo,+ yemwe mayi ake anali mkazi wa Uriya.
-
Luka 3:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
mwana wa Obedi,+
mwana wa Boazi,+
mwana wa Salimoni,+
mwana wa Naasoni,+
-
-
-