Hoseya 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno ndinakupatsa mfumu nditakwiya+ ndipo ndidzaichotsa nditakwiya.+