1 Samueli 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Poyankha, Yehova anauza Samueli+ kuti: “Mvera zonse zimene anthuwo akunena kwa iwe,+ pakuti sanakane iweyo koma akana ine kuti ndisakhale mfumu yawo.+ 1 Samueli 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano mfumu imene mwasankha ndi imeneyi, mfumu imene mwapempha.+ Ndipotu Yehova wakuikiranidi mfumu+ yoti izikulamulirani.
7 Poyankha, Yehova anauza Samueli+ kuti: “Mvera zonse zimene anthuwo akunena kwa iwe,+ pakuti sanakane iweyo koma akana ine kuti ndisakhale mfumu yawo.+
13 Tsopano mfumu imene mwasankha ndi imeneyi, mfumu imene mwapempha.+ Ndipotu Yehova wakuikiranidi mfumu+ yoti izikulamulirani.