1 Samueli 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma mukachita zinthu zoipa mouma khosi, mudzasesedwa,+ inu pamodzi ndi mfumu yanuyo.”+ Yeremiya 52:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mfumu ya Babulo inachititsa khungu Zedekiya+ ndipo kenako inamumanga ndi maunyolo amkuwa n’kupita naye ku Babulo.+ Kumeneko anamuika m’ndende mpaka tsiku la imfa yake.
11 Mfumu ya Babulo inachititsa khungu Zedekiya+ ndipo kenako inamumanga ndi maunyolo amkuwa n’kupita naye ku Babulo.+ Kumeneko anamuika m’ndende mpaka tsiku la imfa yake.