1 Samueli 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye anatumadi munthu kukam’tenga. Mnyamatayo anali wamaonekedwe ofiirira,+ mnyamata wa maso okongola, ndiponso wooneka bwino. Pamenepo Yehova anati: “Ndi ameneyu! Nyamuka umudzoze.”+ 2 Samueli 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako amuna a ku Yuda+ anabwera ndi kudzoza+ Davide kumeneko kukhala mfumu ya nyumba ya Yuda.+ Ndiyeno anthu anauza Davide kuti: “Anthu a ku Yabesi-giliyadi ndi amene anaika Sauli m’manda.” Salimo 89:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndapeza Davide mtumiki wanga,+Ndipo ndamudzoza ndi mafuta anga opatulika.+
12 Iye anatumadi munthu kukam’tenga. Mnyamatayo anali wamaonekedwe ofiirira,+ mnyamata wa maso okongola, ndiponso wooneka bwino. Pamenepo Yehova anati: “Ndi ameneyu! Nyamuka umudzoze.”+
4 Kenako amuna a ku Yuda+ anabwera ndi kudzoza+ Davide kumeneko kukhala mfumu ya nyumba ya Yuda.+ Ndiyeno anthu anauza Davide kuti: “Anthu a ku Yabesi-giliyadi ndi amene anaika Sauli m’manda.”