1 Samueli 17:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Mfilisitiyo ataona Davide, anayamba kumuderera+ chifukwa anali mnyamata+ wamaonekedwe ofiirira,+ ndiponso wokongola.+ Nyimbo ya Solomo 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Wachikondi wanga ndi wokongola ndipo khungu lake ndi lofiirira. Pa amuna 10,000, iye ndiye wooneka bwino kwambiri.+ Maliro 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anaziri+ ake anali oyera kuposa chipale chofewa.+ Analinso oyera kuposa mkaka.Ndipotu anali ofiira+ kuposa miyala yamtengo wapatali ya korali. Analinso osalala ngati mwala wa safiro.+
42 Mfilisitiyo ataona Davide, anayamba kumuderera+ chifukwa anali mnyamata+ wamaonekedwe ofiirira,+ ndiponso wokongola.+
10 “Wachikondi wanga ndi wokongola ndipo khungu lake ndi lofiirira. Pa amuna 10,000, iye ndiye wooneka bwino kwambiri.+
7 Anaziri+ ake anali oyera kuposa chipale chofewa.+ Analinso oyera kuposa mkaka.Ndipotu anali ofiira+ kuposa miyala yamtengo wapatali ya korali. Analinso osalala ngati mwala wa safiro.+