1 Samueli 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye anatumadi munthu kukam’tenga. Mnyamatayo anali wamaonekedwe ofiirira,+ mnyamata wa maso okongola, ndiponso wooneka bwino. Pamenepo Yehova anati: “Ndi ameneyu! Nyamuka umudzoze.”+ Nyimbo ya Solomo 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Wachikondi wanga ndi wokongola ndipo khungu lake ndi lofiirira. Pa amuna 10,000, iye ndiye wooneka bwino kwambiri.+
12 Iye anatumadi munthu kukam’tenga. Mnyamatayo anali wamaonekedwe ofiirira,+ mnyamata wa maso okongola, ndiponso wooneka bwino. Pamenepo Yehova anati: “Ndi ameneyu! Nyamuka umudzoze.”+
10 “Wachikondi wanga ndi wokongola ndipo khungu lake ndi lofiirira. Pa amuna 10,000, iye ndiye wooneka bwino kwambiri.+