Deuteronomo 32:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Kondwerani, mitundu inu, pamodzi ndi anthu ake,+Pakuti adzabwezera magazi a atumiki ake,+Ndipo adzabwezera chilango kwa adani ake,+Nadzaphimba machimo a dziko la anthu ake.” Salimo 18:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 N’chifukwa chake ndidzakutamandani, inu Yehova pakati pa mitundu.+Ndipo ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.+ Salimo 117:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 117 Tamandani Yehova, inu mitundu yonse ya anthu.+Mulemekezeni, inu mafuko onse.+ Aroma 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 kuti mitundu ina+ ipereke ulemerero kwa Mulungu chifukwa cha chifundo+ chake, monga mmene Malemba amanenera kuti: “N’chifukwa chake ndidzakuvomerezani poyera pakati pa mitundu. Ndipo ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.”+
43 Kondwerani, mitundu inu, pamodzi ndi anthu ake,+Pakuti adzabwezera magazi a atumiki ake,+Ndipo adzabwezera chilango kwa adani ake,+Nadzaphimba machimo a dziko la anthu ake.”
49 N’chifukwa chake ndidzakutamandani, inu Yehova pakati pa mitundu.+Ndipo ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.+
9 kuti mitundu ina+ ipereke ulemerero kwa Mulungu chifukwa cha chifundo+ chake, monga mmene Malemba amanenera kuti: “N’chifukwa chake ndidzakuvomerezani poyera pakati pa mitundu. Ndipo ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.”+