Genesis 25:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Amenewa ndiwo ana a Isimaeli, potsata mayina awo, malinga ndi midzi yawo ndi misasa yawo yotchinga ndi mipanda.+ Anali atsogoleri okwanira 12 malinga ndi mafuko awo.+ Numeri 25:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Dzina la mkazi wachimidiyani amene anaphedwayo linali Kozibi, mwana wa Zuri.+ Zuri anali mtsogoleri wa fuko la nyumba ina ya makolo ku Midiyani.+
16 Amenewa ndiwo ana a Isimaeli, potsata mayina awo, malinga ndi midzi yawo ndi misasa yawo yotchinga ndi mipanda.+ Anali atsogoleri okwanira 12 malinga ndi mafuko awo.+
15 Dzina la mkazi wachimidiyani amene anaphedwayo linali Kozibi, mwana wa Zuri.+ Zuri anali mtsogoleri wa fuko la nyumba ina ya makolo ku Midiyani.+