Aroma 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Komanso kuti anthu a mitundu ina alemekeze Mulungu chifukwa cha chifundo chake,+ mogwirizana ndi zimene Malemba amanena kuti: “Nʼchifukwa chake ndidzakulemekezani pakati pa mitundu ya anthu ndipo ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.”+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:9 Nsanja ya Olonda,7/1/1997, ptsa. 18-19
9 Komanso kuti anthu a mitundu ina alemekeze Mulungu chifukwa cha chifundo chake,+ mogwirizana ndi zimene Malemba amanena kuti: “Nʼchifukwa chake ndidzakulemekezani pakati pa mitundu ya anthu ndipo ndidzaimba nyimbo zotamanda dzina lanu.”+