Deuteronomo 32:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Inu anthu a mitundu ina, sangalalani limodzi ndi anthu ake,+Chifukwa adzabwezera magazi a atumiki ake,+Ndipo adzabwezera chilango kwa adani ake,+Komanso adzaphimba machimo a dziko la anthu ake.”* Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:43 Nsanja ya Olonda,2/1/1998, ptsa. 12, 174/15/1991, ptsa. 12-13
43 Inu anthu a mitundu ina, sangalalani limodzi ndi anthu ake,+Chifukwa adzabwezera magazi a atumiki ake,+Ndipo adzabwezera chilango kwa adani ake,+Komanso adzaphimba machimo a dziko la anthu ake.”*