1 Mbiri 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Muimbireni,+ muimbireni nyimbo zomutamanda!+Sinkhasinkhani ntchito zake zonse zodabwitsa.+ Salimo 145:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzakutamandani tsiku lonse.+Ndidzatamanda dzina lanu mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+ Salimo 146:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzatamanda Yehova pamene ndili moyo.+Ndidzaimbira Mulungu wanga nyimbo zomutamanda kwa moyo wanga wonse.+
2 Ndidzatamanda Yehova pamene ndili moyo.+Ndidzaimbira Mulungu wanga nyimbo zomutamanda kwa moyo wanga wonse.+