Salimo 71:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Inu Mulungu, mwandiphunzitsa kuyambira pa unyamata wanga,+Ndipo mpaka pano ndikunena za ntchito zanu zodabwitsa.+ Salimo 107:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Wanzeru ndani? Iye aona zimenezi,+Ndi kuchita chidwi ndi ntchito za Yehova zosonyeza kukoma mtima kwake kosatha.+
17 Inu Mulungu, mwandiphunzitsa kuyambira pa unyamata wanga,+Ndipo mpaka pano ndikunena za ntchito zanu zodabwitsa.+
43 Wanzeru ndani? Iye aona zimenezi,+Ndi kuchita chidwi ndi ntchito za Yehova zosonyeza kukoma mtima kwake kosatha.+