2 Samueli 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Davide analankhula ndi Yehova mawu a nyimbo iyi,+ pa tsiku limene Yehova anamulanditsa kwa adani ake+ onse ndiponso m’manja mwa Sauli.+ 1 Mbiri 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno Davide anaika Alevi+ ena kukhala otumikira+ pa likasa la Yehova kuti azikumbutsa+ anthu, kuyamika,+ ndi kutamanda+ Yehova Mulungu wa Isiraeli. Salimo 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndidzakutamandani inu Yehova ndi mtima wanga wonse.+Ndidzalengeza ntchito zanu zonse zodabwitsa.+ Salimo 66:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Bwerani, mvetserani, inu nonse oopa Mulungu, ndipo ine ndifotokoza+Zimene wandichitira.+
22 Davide analankhula ndi Yehova mawu a nyimbo iyi,+ pa tsiku limene Yehova anamulanditsa kwa adani ake+ onse ndiponso m’manja mwa Sauli.+
4 Ndiyeno Davide anaika Alevi+ ena kukhala otumikira+ pa likasa la Yehova kuti azikumbutsa+ anthu, kuyamika,+ ndi kutamanda+ Yehova Mulungu wa Isiraeli.