-
Salimo 86:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Ndikukutamandani inu Yehova Mulungu wanga ndi mtima wanga wonse,+
Ndipo ndidzalemekeza dzina lanu mpaka kalekale,
-