Salimo 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndidzakutamandani inu Yehova ndi mtima wanga wonse.+Ndidzalengeza ntchito zanu zonse zodabwitsa.+ Salimo 107:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu ayamike Yehova chifukwa cha kukoma mtima kwake kosatha,+Ndiponso chifukwa cha ntchito zake zodabwitsa zimene wachitira ana a anthu.+ Salimo 138:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 138 Ndidzakutamandani ndi mtima wanga wonse.+Ndidzakuimbirani nyimbo zokutamandani pamaso pa milungu ina.+
8 Anthu ayamike Yehova chifukwa cha kukoma mtima kwake kosatha,+Ndiponso chifukwa cha ntchito zake zodabwitsa zimene wachitira ana a anthu.+
138 Ndidzakutamandani ndi mtima wanga wonse.+Ndidzakuimbirani nyimbo zokutamandani pamaso pa milungu ina.+