Yobu 19:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Amuna onse amene anali anzanga apamtima akudana nane,+Ndipo amene ndinali kuwakonda anditembenukira.+ Salimo 89:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mulungu ayenera kuopedwa pakati pa gulu lake la oyera.+Iye ndi wamkulu ndi wochititsa mantha kuposa onse omuzungulira.+
19 Amuna onse amene anali anzanga apamtima akudana nane,+Ndipo amene ndinali kuwakonda anditembenukira.+
7 Mulungu ayenera kuopedwa pakati pa gulu lake la oyera.+Iye ndi wamkulu ndi wochititsa mantha kuposa onse omuzungulira.+