Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 1:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Pansi pa thambolo, mapiko awo anali otambasuka. Phiko lililonse linagundana ndi phiko la chamoyo chinzake. Chamoyo chilichonse chinali ndi mapiko awiri ochiphimba mbali imodzi, ndi mapiko ena awiri ochiphimba mbali ina ya thupi lake.

  • Danieli 7:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mtsinje wa moto unali kuyenda kuchokera kwa iye.+ Panali atumiki okwana miliyoni imodzi amene anali kumutumikira nthawi zonse,+ ndi atumiki enanso mamiliyoni 100 amene anali kuimirira pamaso pake nthawi zonse.+ Bwalo la milandu+ linakhala pansi, ndipo mabuku anatsegulidwa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena