Salimo 76:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu ndinu wochititsa mantha,+Ndani angaime pamaso panu inu mutakwiya kwambiri?+ Yesaya 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamwamba pake panali aserafi.+ Mserafi aliyense anali ndi mapiko 6. Mapiko awiri anaphimbira nkhope yake,+ awiri anaphimbira mapazi ake ndipo awiri anali kuulukira.
2 Pamwamba pake panali aserafi.+ Mserafi aliyense anali ndi mapiko 6. Mapiko awiri anaphimbira nkhope yake,+ awiri anaphimbira mapazi ake ndipo awiri anali kuulukira.