Ekisodo 14:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Isiraeli anaonanso dzanja lamphamvu limene Yehova anagonjetsa nalo Aiguputo. Pamenepo Aisiraeli anayamba kuopa Yehova ndi kukhulupirira Yehova ndi mtumiki wake Mose.+ Salimo 89:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mulungu ayenera kuopedwa pakati pa gulu lake la oyera.+Iye ndi wamkulu ndi wochititsa mantha kuposa onse omuzungulira.+
31 Isiraeli anaonanso dzanja lamphamvu limene Yehova anagonjetsa nalo Aiguputo. Pamenepo Aisiraeli anayamba kuopa Yehova ndi kukhulupirira Yehova ndi mtumiki wake Mose.+
7 Mulungu ayenera kuopedwa pakati pa gulu lake la oyera.+Iye ndi wamkulu ndi wochititsa mantha kuposa onse omuzungulira.+