Salimo 76:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu nokha ndinu wochititsa mantha.+ Ndi ndani angapirire mkwiyo wanu waukulu?+