Salimo 89:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mulungu ndi wochititsa mantha komanso wolemekezeka pakati pa gulu lake la oyera.*+Iye ndi wamkulu komanso wochititsa mantha kwa onse amene amuzungulira.+
7 Mulungu ndi wochititsa mantha komanso wolemekezeka pakati pa gulu lake la oyera.*+Iye ndi wamkulu komanso wochititsa mantha kwa onse amene amuzungulira.+