Yesaya 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamenepo mserafi mmodzi anaulukira kwa ine. M’manja mwake munali khala lamoto+ limene analitenga paguwa lansembe ndi chopanira.+
6 Pamenepo mserafi mmodzi anaulukira kwa ine. M’manja mwake munali khala lamoto+ limene analitenga paguwa lansembe ndi chopanira.+