Chivumbulutso 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma nthawi yomweyo, mngeloyo anatenga chiwiya chofukiziramo chija, n’kudzazamo moto+ umene anapala paguwa lansembe, ndi kuuponyera kudziko lapansi.+ Ndiyeno kunagunda mabingu,+ kunamveka mawu, ndipo kunachita mphezi+ ndi chivomezi.+
5 Koma nthawi yomweyo, mngeloyo anatenga chiwiya chofukiziramo chija, n’kudzazamo moto+ umene anapala paguwa lansembe, ndi kuuponyera kudziko lapansi.+ Ndiyeno kunagunda mabingu,+ kunamveka mawu, ndipo kunachita mphezi+ ndi chivomezi.+