Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 15:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Mphamvu ndi nyonga yanga ndi Ya,*+ pakuti wandipulumutsa.+

      Ameneyu ndi Mulungu wanga, ndidzam’tamanda.+ Ndiye Mulungu wa atate anga,+ ndidzam’kweza.+

  • Salimo 35:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ndidzakutamandani mu mpingo waukulu.+

      Ndidzakutamandani pakati pa anthu ambiri.+

  • Salimo 68:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Anthu inu, imbirani Mulungu, muimbireni nyimbo zotamanda dzina lake.+

      Muimbireni nyimbo Iye amene akudutsa m’chipululu,+

      Amene dzina lake ndi Ya,*+ ndipo kondwerani pamaso pake.

  • Salimo 113:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 113 Tamandani Ya, anthu inu!+

      Inu atumiki a Yehova, mutamandeni,+

      Tamandani dzina la Yehova.+

  • Chivumbulutso 19:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Zimenezi zitatha, ndinamva mawu ofuula kumwamba+ ngati mawu a khamu lalikulu, akuti: “Tamandani Ya,* anthu inu!+ Chipulumutso,+ ulemerero, ndi mphamvu ndi za Mulungu wathu,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena