Salimo 67:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mitundu ya anthu isangalale ndi kufuula mokondwera,+Pakuti inu mudzaweruza anthu molungama.+Ndipo mudzatsogolera mitundu ya anthu padziko lapansi. [Seʹlah.] Yesaya 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 M’tsiku limenelo mudzanenadi kuti: “Yamikani Yehova anthu inu.+ Itanani pa dzina lake.+ Dziwitsani mitundu ya anthu zochita zake.+ Nenani kuti dzina lake n’lokwezeka.+
4 Mitundu ya anthu isangalale ndi kufuula mokondwera,+Pakuti inu mudzaweruza anthu molungama.+Ndipo mudzatsogolera mitundu ya anthu padziko lapansi. [Seʹlah.]
4 M’tsiku limenelo mudzanenadi kuti: “Yamikani Yehova anthu inu.+ Itanani pa dzina lake.+ Dziwitsani mitundu ya anthu zochita zake.+ Nenani kuti dzina lake n’lokwezeka.+