Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 9:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Iye adzaweruza anthu padziko lapansi mwachilungamo.+

      Adzazenga mlandu mitundu ya anthu moyenerera.+

  • Salimo 96:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Nenani pakati pa anthu a mitundu ina kuti: “Yehova wakhala mfumu.+

      Dziko lapansi nalonso lakhazikika moti silingagwedezeke.+

      Iye adzaweruzira mitundu ya anthu milandu yawo mwachilungamo.”+

  • Salimo 98:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Pakuti iye wabwera kudzaweruza dziko lapansi.+

      Adzaweruza dziko mwachilungamo,+

      Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu molungama.+

  • Aroma 2:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Koma chifukwa chakuti ndiwe wosafuna kusintha khalidwe+ ndiponso wa mtima wosalapa,+ ukudzisungira mkwiyo wa Mulungu.+ Mulungu adzasonyeza mkwiyo+ umenewu pa tsiku loulula+ chiweruzo chake cholungama.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena