Salimo 96:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Lengezani pakati pa anthu a mitundu ina kuti: “Yehova wakhala Mfumu.+ Dziko lapansi lakhazikika moti silingasunthidwe.* Iye adzaweruza mitundu ya anthu mwachilungamo.”*+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 96:10 Nsanja ya Olonda,5/15/1990, tsa. 5
10 Lengezani pakati pa anthu a mitundu ina kuti: “Yehova wakhala Mfumu.+ Dziko lapansi lakhazikika moti silingasunthidwe.* Iye adzaweruza mitundu ya anthu mwachilungamo.”*+