Salimo 96:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nenani pakati pa anthu a mitundu ina kuti: “Yehova wakhala mfumu.+Dziko lapansi nalonso lakhazikika moti silingagwedezeke.+Iye adzaweruzira mitundu ya anthu milandu yawo mwachilungamo.”+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 96:10 Nsanja ya Olonda,5/15/1990, tsa. 5
10 Nenani pakati pa anthu a mitundu ina kuti: “Yehova wakhala mfumu.+Dziko lapansi nalonso lakhazikika moti silingagwedezeke.+Iye adzaweruzira mitundu ya anthu milandu yawo mwachilungamo.”+