Salimo 93:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 93 Yehova wakhala mfumu!+Iye wavala ulemerero.+Yehova wavala mphamvu ngati chovala, ndipo wamangirira mphamvuzo m’chiuno mwake.+Dziko lapansi lakhazikika, moti silingagwedezeke.+ Salimo 97:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 97 Yehova wakhala mfumu!+ Dziko lapansi likondwere,+Ndipo zilumba zambiri zisangalale.+ Chivumbulutso 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mngelo wa 7 analiza lipenga+ lake. Ndipo kumwamba kunamveka mawu osiyanasiyana, akunena mokweza kuti: “Ufumu wa dziko wakhala ufumu wa Ambuye wathu+ ndi wa Khristu wake.+ Iye adzalamulira monga mfumu kwamuyaya.”+ Chivumbulutso 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako ndinamva mawu ngati a khamu lalikulu, omveka ngati mkokomo wa madzi ambiri ndi mabingu amphamvu. Mawuwo anati: “Tamandani Ya,+ anthu inu, chifukwa Yehova* Mulungu wathu, Wamphamvuyonse,+ wayamba kulamulira monga mfumu.+
93 Yehova wakhala mfumu!+Iye wavala ulemerero.+Yehova wavala mphamvu ngati chovala, ndipo wamangirira mphamvuzo m’chiuno mwake.+Dziko lapansi lakhazikika, moti silingagwedezeke.+
15 Mngelo wa 7 analiza lipenga+ lake. Ndipo kumwamba kunamveka mawu osiyanasiyana, akunena mokweza kuti: “Ufumu wa dziko wakhala ufumu wa Ambuye wathu+ ndi wa Khristu wake.+ Iye adzalamulira monga mfumu kwamuyaya.”+
6 Kenako ndinamva mawu ngati a khamu lalikulu, omveka ngati mkokomo wa madzi ambiri ndi mabingu amphamvu. Mawuwo anati: “Tamandani Ya,+ anthu inu, chifukwa Yehova* Mulungu wathu, Wamphamvuyonse,+ wayamba kulamulira monga mfumu.+