Salimo 96:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nenani pakati pa anthu a mitundu ina kuti: “Yehova wakhala mfumu.+Dziko lapansi nalonso lakhazikika moti silingagwedezeke.+Iye adzaweruzira mitundu ya anthu milandu yawo mwachilungamo.”+ Salimo 97:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 97 Yehova wakhala mfumu!+ Dziko lapansi likondwere,+Ndipo zilumba zambiri zisangalale.+ Yesaya 52:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mapazi+ a munthu yemwe akuyenda pamwamba pa mapiri pobweretsa uthenga wabwino, ndi okongola kwabasi!+ Munthu yemwe akulengeza za mtendere,+ yemwe akubweretsa uthenga wabwino wa zinthu zabwino kuposa kale,+ yemwe akulengeza za chipulumutso,+ yemwe akuuza Ziyoni kuti: “Mulungu wako wakhala mfumu.”+ Chivumbulutso 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 ndi mawu akuti: “Tikukuyamikani+ inu Yehova, Mulungu Wamphamvuyonse,+ Inu amene mulipo+ ndi amene munalipo, chifukwa mwatenga mphamvu yanu yaikulu+ ndi kuyamba kulamulira monga mfumu.+ Chivumbulutso 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako ndinamva mawu ngati a khamu lalikulu, omveka ngati mkokomo wa madzi ambiri ndi mabingu amphamvu. Mawuwo anati: “Tamandani Ya,+ anthu inu, chifukwa Yehova* Mulungu wathu, Wamphamvuyonse,+ wayamba kulamulira monga mfumu.+
10 Nenani pakati pa anthu a mitundu ina kuti: “Yehova wakhala mfumu.+Dziko lapansi nalonso lakhazikika moti silingagwedezeke.+Iye adzaweruzira mitundu ya anthu milandu yawo mwachilungamo.”+
7 Mapazi+ a munthu yemwe akuyenda pamwamba pa mapiri pobweretsa uthenga wabwino, ndi okongola kwabasi!+ Munthu yemwe akulengeza za mtendere,+ yemwe akubweretsa uthenga wabwino wa zinthu zabwino kuposa kale,+ yemwe akulengeza za chipulumutso,+ yemwe akuuza Ziyoni kuti: “Mulungu wako wakhala mfumu.”+
17 ndi mawu akuti: “Tikukuyamikani+ inu Yehova, Mulungu Wamphamvuyonse,+ Inu amene mulipo+ ndi amene munalipo, chifukwa mwatenga mphamvu yanu yaikulu+ ndi kuyamba kulamulira monga mfumu.+
6 Kenako ndinamva mawu ngati a khamu lalikulu, omveka ngati mkokomo wa madzi ambiri ndi mabingu amphamvu. Mawuwo anati: “Tamandani Ya,+ anthu inu, chifukwa Yehova* Mulungu wathu, Wamphamvuyonse,+ wayamba kulamulira monga mfumu.+