Salimo 69:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kumwamba ndi dziko lapansi zimutamande,+Chimodzimodzinso nyanja ndi chilichonse choyenda mmenemo.+ Yesaya 49:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Fuulani mokondwa kumwamba inu,+ ndipo sangalala iwe dziko lapansi.+ Mapiri asangalale ndipo afuule ndi chisangalalo.+ Pakuti Yehova watonthoza anthu ake+ ndipo amamvera chisoni anthu ake osautsidwa.+
34 Kumwamba ndi dziko lapansi zimutamande,+Chimodzimodzinso nyanja ndi chilichonse choyenda mmenemo.+
13 Fuulani mokondwa kumwamba inu,+ ndipo sangalala iwe dziko lapansi.+ Mapiri asangalale ndipo afuule ndi chisangalalo.+ Pakuti Yehova watonthoza anthu ake+ ndipo amamvera chisoni anthu ake osautsidwa.+