Salimo 98:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Fuulirani Yehova mosangalala chifukwa wapambana, inu nonse anthu a padziko lapansi.+Kondwerani, fuulani mosangalala ndi kuimba nyimbo zomutamanda.+ Yesaya 42:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Imbirani Yehova nyimbo yatsopano.+ M’tamandeni kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+ M’tamandeni inu amuna amene mumadalira nyanja+ ndi zonse zokhala mmenemo, ndiponso inu zilumba ndi anthu okhala m’zilumbazo.+
4 Fuulirani Yehova mosangalala chifukwa wapambana, inu nonse anthu a padziko lapansi.+Kondwerani, fuulani mosangalala ndi kuimba nyimbo zomutamanda.+
10 Imbirani Yehova nyimbo yatsopano.+ M’tamandeni kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+ M’tamandeni inu amuna amene mumadalira nyanja+ ndi zonse zokhala mmenemo, ndiponso inu zilumba ndi anthu okhala m’zilumbazo.+