Salimo 96:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 96 Imbirani Yehova nyimbo yatsopano.+Imbirani Yehova, inu anthu nonse okhala padziko lapansi.+ Salimo 98:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 98 IMBIRANI Yehova nyimbo yatsopano,+Pakuti zimene wachita ndi zodabwitsa.+Dzanja lake lamanja, ndithu mkono wake woyera, wabweretsa chipulumutso.+ Chivumbulutso 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo anali kuimba+ nyimbo yokhala ngati yatsopano+ pamaso pa mpando wachifumu, pamaso pa zamoyo zinayi,+ ndi pamaso pa akulu.+ Palibe anatha kuiphunzira nyimboyo, koma 144,000+ amene anagulidwa+ padziko lapansi.
98 IMBIRANI Yehova nyimbo yatsopano,+Pakuti zimene wachita ndi zodabwitsa.+Dzanja lake lamanja, ndithu mkono wake woyera, wabweretsa chipulumutso.+
3 Iwo anali kuimba+ nyimbo yokhala ngati yatsopano+ pamaso pa mpando wachifumu, pamaso pa zamoyo zinayi,+ ndi pamaso pa akulu.+ Palibe anatha kuiphunzira nyimboyo, koma 144,000+ amene anagulidwa+ padziko lapansi.