Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 15:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndi mulungu wina uti amene angafanane nanu, inu Yehova?+

      Ndinu woyera kopambana, ndani angafanane ndi inu?+

      Ndinu woyenera kuopedwa+ ndi kukuimbirani nyimbo zotamanda.+ Inu ndinu wochita zodabwitsa.+

  • Salimo 77:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Inu ndinu Mulungu woona amene mukuchita zodabwitsa.+

      Mphamvu zanu mwazidziwikitsa pakati pa mitundu ya anthu.+

  • Salimo 86:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti inu ndinu wamkulu ndipo mukuchita zinthu zodabwitsa.+

      Inu nokha ndinu Mulungu.+

  • Salimo 105:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Kumbukirani ntchito zodabwitsa zimene wachita,+

      Kumbukirani zozizwitsa zake ndi zigamulo zotuluka m’kamwa mwake,+

  • Salimo 111:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Ntchito za Yehova ndi zazikulu,+

      ד [Daʹleth]

      Onse amene amasangalala nazo amazisinkhasinkha.+

  • Salimo 136:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Yamikani Wochita zodabwitsa ndiponso ntchito zazikulu:+

      Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+

  • Luka 1:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Chifukwa Wamphamvuyo wandichitira zazikulu, ndipo dzina lake ndi loyera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena